Hymn 730 A! Yesu mwapangana treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 730 A! Yesu mwapangana A! Yesu mwapangana Ndi anthu anuwo Adzakhala ndinu Ku Dziko lanulo; Inenso ndapangana Ndisabwerere ‘yi; Mndipatse mphamvu yanu Ambuye ndinudi.