Hymn 479 Munanena mulandira December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 479 Munanena mulandira Munanena mulandira Osauka ndi oipa; Inu ndinu wachifundo Ndi wamphamvu yolanditsa; Yesu wathu, Yesu wathu, Tidzatu tiana tanu.