Hymn 479 Munanena mulandira treasurehymns 9 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 479 Munanena mulandira Munanena mulandira Osauka ndi oipa; Inu ndinu wachifundo Ndi wamphamvu yolanditsa; Yesu wathu, Yesu wathu, Tidzatu tiana tanu.