Hymn 1163 Tili ndi mtendere December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1163 Tili ndi mtendere Tili ndi mtendere Wopambanatu, Monga ngati mtsinje Mumitimamo; Koma mtsinje uno Umayenda phee, Nthawi zonse mtima Nutonthozabe.