Hymn 1163 Tili ndi mtendere treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1163 Tili ndi mtendere Tili ndi mtendere Wopambanatu, Monga ngati mtsinje Mumitimamo; Koma mtsinje uno Umayenda phee, Nthawi zonse mtima Nutonthozabe.