Hymn 1108 Khala chete mtima wanga, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1108 Khala chete mtima wanga, Khala chete mtima wanga, Zikwanire zinthu zako; Usakhumbe zapansipa, Koma Mlungu wako yekha.