Hymn 1108 Khala chete mtima wanga, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1108 Khala chete mtima wanga, Khala chete mtima wanga, Zikwanire zinthu zako; Usakhumbe zapansipa, Koma Mlungu wako yekha.