Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 294 POYESEDWA ine

  1. Home   »  
  2. Hymn 294 POYESEDWA ine

Hymn 294 POYESEDWA ine

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 294 POYESEDWA ine

 

POYESEDWA ine
Yesu mudzetu,
Mundipempherere
Ndisachimwetu.
Mukaona kuti
Ndilefukatu,
Mbuye mndilimbitse
Nazo mphamvutu.

Ndi zapansi pano
Ndikokedwadi,
Koma ndi chisoni
Mndiphunzitsedi;
Ndisaiŵalire
Za Getsemane,
Pena mtanda wanu
Yesu Mbuye ’Nu.

Mukandipweteka,
Ndipirirapo:
Nsembe yanga ndiyo,
Landirani ’yo.
Ndikachita mantha Sindithaŵa ’yi:
Mtima udzalimba,
Ndidzaima nji!

Pakumalizidwa
Moyo wangawu,
Pomwalira ine,
Mudze Mbuyetu.
Ndidzadzipereka
M’manja mwanumo:
Mpulumutsi Yesu
Mndilandireko.

Post navigation

Previous: Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
Next: Hymn 295 AMBUYE wa Kumwamba,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1286 E, ndikukhulupirani,
  • Hymn 155 Pemphero ndiko kufuna
  • Hymn 325 Walira Yesu wolimbitsayo,
  • Hymn 1108 Khala chete mtima wanga,
  • Hymn 870 Satana apambana tikayamba kusiyana;
  • Hymn 243 Mtima wanga udzakondwera,
  • Hymn 168 Yendani mwaulemerero,
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 1281 Ndikhulupirira, Yesu, mndibvomereko;
  • Hymn 1179 N’kamvera Yesu ndikakondwera,
  • Hymn 1523 Atisangalatsa,
  • Hymn 440 ZIKOMO Ambuye wathu,
  • Hymn 1687 Alonda onsewo
  • Hymn 835 Mukhale ndine, dzuwalo lalowa,
  • Hymn 1332 Imba kawiri ndi kawirinso,
  • Hymn 1603 Zina za Yesu m;Mwambamo,
  • Hymn 142 Kukondwa kwa wodwalayo
  • Hymn 72 Mayi watsogola ku Ulemerero,
  • Hymn 494 YESU Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 939 Ambuye andisunga
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 1435 Ndiwe mlendo lero lino,
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 1026 Inde nditaya chumacho,
  • Hymn 278 Aweruza ndi mphamvu
  • Hymn 1189 Ambuye Mulungu,
  • Hymn 913 Kulibe gombe, nyanja,
  • Hymn 692 Paulendo wathu
  • Hymn 566 Ana inu, ana inu,
  • Hymn 104 M’mene ntchito yathatu,
  • Hymn 1366 Sititha ifedi
  • Hymn 357 Yesu ndiye Mtetezi,
  • Hymn 447 Usachimwe konse,
  • Hymn 1680 Aleluya, Aleluya, Aleluya!
  • Hymn 1395 Mulungu ali nane!
  • Hymn 301 Mwanawankhosa
  • Hymn 385 SINDILI woyenera ’ne,
  • Hymn 1136 Mulungu anditsogolera
  • Hymn 961 Mbuye anatiitana
  • Hymn 1464 Nditama Nsembe ya Mulungu,
  • Hymn 225 Yesu akhazika
  • Hymn 1334 Walandira inetu
  • Hymn 146 Inu ndidzatama
  • Hymn 1651 Kwa Mulungu m’Mwambamo
  • Hymn 315 Munagwa pa Atumwiwo;
  • Hymn 169 ’MVANI liu lomwe
  • Hymn 211 TIDZALAKALAKA kuwonana naye,
  • Hymn 825 Mpatse ana ‘ng’ono
  • Hymn 1052 Ndilira mtima wotamanda
  • Hymn 1838 Ndiye Mbuye wa ambuye;
  • Hymn 371 AMBUYE, tasonkhana
  • Hymn 326 Yesu, Bwenzi la ochimwa,
  • Hymn 76 E, MOYO wanga’we
  • Hymn 1633 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 177 ŴALIRA Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 330 Yesu ndiye Mtsogoleri
  • Hymn 206 Uzanitu abale,
  • Hymn 674 Anthu onse taukani,
  • Hymn 192 ZAKEYU mkulu wa misonkho,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version