Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,

  1. Home   »  
  2. Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,

Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,

 

MAVUTO ndi ambiri,
Padziko lapansi;
Koma tikalimbikatu,
Tikapumula
M’mwambamo.

(M) Yendani,
(O) Yendanibe,
(M) Munjira,
(O) Njira ya moyo,
Koma tikalimbikatu,
Tikapumula
M’mwambamo.

Adani ndi ambiri,
Padziko lapansi;
Koma tikalimbikatu,
Tikapumula
M’mwambamo.

Mayesero alipo,
Padziko lapansi;
Koma tikalimbikatu,
Tikapumula
M’mwambamo.

Post navigation

Previous: Hymn 283 AMBUYE m’chipululu,
Next: Hymn 285 DZIKO lino lapansi,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 791 Anthu opembedzawo
  • Hymn 1084 “Khala mwa Ine,” munachotsa tsoka,
  • Hymn 98 Ndidzamwona maso ndi maso
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 475 MZINDA woyerawo
  • Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli
  • Hymn 238 MULUNGU wanga,
  • Hymn 613 Dziko lonse nla Mulungu
  • Hymn 96 MTIMA wanga uyamiketu,
  • Hymn 481 Yesu wa Kumwamba,
  • Hymn 1720 Padzanja lachifundolo
  • Hymn 1315 Ambuye ‘naitana ‘ne:
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 703 Dzuwa, madzi, kudya, mpweya,
  • Hymn 1475 Anathera pamtanda zintchito zonsezi
  • Hymn 17 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 1748 Ambuye tsopano lino,
  • Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo
  • Hymn 818 Mkhululukire,
  • Hymn 688 Anthu akum’mawa
  • Hymn 682 Tsatani Mbuye Yesuyo ndi mtanda wakewo;
  • Hymn 270 Zoopsya zopambana
  • Hymn 116 MBUYE, Mawu anu
  • Hymn 1029 Nkhawa tilibe; Yesuyo
  • Hymn 212 NDI MISOZI, ndi chisoni,
  • Hymn 492 DZIKO lilipolo
  • Hymn 836 Kamoyo kanga katha lero lino,
  • Hymn 147 Ndisauka, ndinachimwa,
  • Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
  • Hymn 992 Mukandipweteka,
  • Hymn 1105 Khala chete mtima wanga
  • Hymn 932 Munabvala thupi lathu,
  • Hymn 322 PAKUYITANIDWA munthu pa dziko ino,
  • Hymn 133 NSEMBE yake ya Kaini,
  • Hymn 211 TIDZALAKALAKA kuwonana naye,
  • Hymn 242 NDIIMBA mumtima mokondwa,
  • Hymn 1379 Mulungu yemweyo
  • Hymn 33 Tamandani Mbuye,
  • Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
  • Hymn 142 Kukondwa kwa wodwalayo
  • Hymn 1689 Dzukani nayetu,
  • Hymn 358 Dzina lake Yesuyo,
  • Hymn 1640 Alinkudza Ambuye Yesu
  • Hymn 87 IDZANI nonse ’nu
  • Hymn 1794 Mulungu awakonda anthu
  • Hymn 1763 Amithenga anaimba
  • Hymn 819 Lero tigone,
  • Hymn 1690 Titama Yesuyo,
  • Hymn 259 Zoipa zakanikadi,
  • Hymn 1427 Penyetsetsa Yesu,
  • Hymn 977 Musagonje, anthu inu,
  • Hymn 1417 Atate ‘nu, atate ‘nu,
  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,
  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 746 Imfa ndi mdima zinathawa zii!
  • Hymn 1181 Adalitsika munthuyo
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version