Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

  1. Home   »  
  2. Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

 

KUNALI munthu ku Yeriko,
Dzina lake Zakeyu;
Anali munthu wamkulu,
Wokhometsa misonkho.

(M) Kunali Zakeyu,
(O) Ku Yeriko,
(M) Nafunafuna,
(O) Kuwona Yesu,
(M) Koma chifukwa,
(O) Cha khamulo,
Anakwera mumtengo.

Paulendowo Ambuyeyo,
Anafika pamtengo;
Nayang’ana m’mwamba muja,
Anawona Zakeyu,

Ambuye Yesu nanenadi,
“Fulumira nutsike;
Lero lino ndiyenera,
Kukhala m’nyumba mwako.”

Zakoyuyo mofulumira,
Anatsika mumtengo,
Anam’tenga Mbuye Yesu,
Kuti akam’chereze,

Anadandauladi ena,
“Ambuye wachitanji?
Bwanji Iye analowa,
M’nyumba ya wochimwayo?”

Zakeyuyo pakumva ichi,
Anawuza Ambuye:
“Theka la chuma changacho,
Ndidzapatsa osowa.”

Leronso chipulumutsochi,
Chagwera m’nyumba yathu;
Tilape zoipa zathu,
Kutí tipulumuke.

Post navigation

Previous: Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
Next: Hymn 215 TATE ndili mwana wanu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 960 Tilikupita kwathu kuja
  • Hymn 1809 Yampatsa Nowa yemwe,
  • Hymn 671 Mbwere Mlungu Mbuye wathu,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 110 Ndaima nji pa Kristuyo,
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 897 Ndine mlendo pansi pano,
  • Hymn 1582 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 533 Ananu, ziimbani,
  • Hymn 335 Mtembenuke mtima wanu,
  • Hymn 342 Ambiri,
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 910 Nlokoma Dziko langa!
  • Hymn 1125 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
  • Hymn 327 NTCHITO yonse yakeyo
  • Hymn 479 ANYAMATA inutu,
  • Hymn 526 Mnandidzera, Ambuye,
  • Hymn 410 Ana ake angonga
  • Hymn 141 Yenda iwe, yenda,
  • Hymn 282 INU muli mehere,
  • Hymn 279 MBUYE, nditsate bwanjiko?
  • Hymn 319 NDIDZATANI ine,
  • Hymn 402 M’mtima mwangamu mlowemo,
  • Hymn 67 PAMENEPO pokhala madzulo,
  • Hymn 1560 Mthandizi ndinu, mndithangate ine
  • Hymn 316 Ndikhazikike inetu,
  • Hymn 556 Ndani pachimpandocho
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 1134 Pansi pano ndili mlendo,
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 1814 Thupi lamwazi wathu’li
  • Hymn 1638 Alinkudza wansoni Munthu
  • Hymn 711 Ife tonse tichenjere
  • Hymn 71 Andiyembekeza, chinthuchi ndidziwa,
  • Hymn 695 Pomveka konsekonse mbiri
  • Hymn 367 Nonse okhala pansipa,
  • Hymn 250 MBUYANGA Yesu,
  • Hymn 32 YENDANI, Mfumu yamtendere
  • Hymn 152 Inde, Yesu, mundikonda,
  • Hymn 1614 Anabadwa,
  • Hymn 310 MBUYE munditsogolere,
  • Hymn 539 Anafika ‘kazi omwe
  • Hymn 1107 Anthu onse pansi pano
  • Hymn 1096 Tifuna Inu, Mbuye,
  • Hymn 1448 Yesu ndiye Bwenzi lanu,
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 1046 Ndiyere mbuu! E, ndiyere mbuu!
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 1117 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 55 Ambiri tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 1687 Alonda onsewo
  • Hymn 78 Ndipereka zanga zonse,
  • Hymn 268 Potuluka m’mudzimo
  • Hymn 1508 Mundinyemere ‘ne
  • Hymn 179 TUMPHATUMPHA moyo wanga,
  • Hymn 1092 Ndimamva njala kuno, Yesu,
  • Hymn 574 A! Yesu Mbuye wakuyera,
  • Hymn 1709 Pamtandapo Ambuyeyo anafera ifetu,
  • Hymn 139 Bwerani inu nonse, inu nonse,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version