Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,

Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,

 

MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,
Mufike nazo mphamvu zanu zazikuluzo.

Mufike monga nyali younika m’mtimamo.
Mutidziŵitse zakuipa zakukhalamo.

Mufike monga moto wakuotcha zomwezo.
Mutiyeretse ifetu m’mitima mwathumo.

Mufike monga ngati njiŵa yamtenderewo.
Kutitu anthu anu onse akondanetu.

Mufike monga ngati mphepo yokokomayo,
Tikhale tonse nazo mphamvu zanu zonsezo.

Post navigation

Previous: Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,
Next: Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 1328 Ndani afuna kunkako
  • Hymn 443 M’MAŴA tizifesa
  • Hymn 1294 Wakuba uja nachiona,
  • Hymn 1361 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,
  • Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,
  • Hymn 454 Kapena m’mtima ndimakwiya,
  • Hymn 147 Ndisauka, ndinachimwa,
  • Hymn 104 M’mene ntchito yathatu,
  • Hymn 481 Yesu wa Kumwamba,
  • Hymn 90 WINA atikonda ife,
  • Hymn 1425 Apempha malo Ambuye;
  • Hymn 1478 Azizwa anthu ajawo,
  • Hymn 417 M’BWERE Mlungu Mbuye wathu,
  • Hymn 1200 Ambuye, m’imfamo
  • Hymn 423 MUNENE Mbuye, ’nenetu,
  • Hymn 709 Munthu aganize
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 1302 Ndi inetu sinditha ‘yi
  • Hymn 1824 Mulungu wathu Mmodzi yekha
  • Hymn 1734 “Senzani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 1661 Ndimachitira
  • Hymn 950 Sindidapempha kale Mbuye ‘yi,
  • Hymn 759 Ndilawako tsopanoli
  • Hymn 1690 Titama Yesuyo,
  • Hymn 388 Ambuye, Mzimu wanu
  • Hymn 182 YESU watidzera, watidzera,
  • Hymn 1203 Zambiri zangazo
  • Hymn 728 A! Yesu, ndapangana
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 434 Zondipingitsa zonse
  • Hymn 117 CHOLIMBITSA mtima ndi chonditsogolera;
  • Hymn 1480 Afika Yesu leroli,
  • Hymn 204 NDASIYA zonse ndi Yesu kalelo,
  • Hymn 82 YANG’ANANI, anthu onse,
  • Hymn 602 Mpulumutsi wakukoma,
  • Hymn 520 Tamva tikondane naye,
  • Hymn 1069 Zochimwa zathu m’mtimamo
  • Hymn 175 Mlungu mverani, mphamvu patseni,
  • Hymn 118 PANALI munthu amene,
  • Hymn 1756 Mwana, adzakuyesa
  • Hymn 1163 Tili ndi mtendere
  • Hymn 646 Mudalitse nyumba yathu;
  • Hymn 96 Kodi mudzampembedza Mbuye
  • Hymn 597 Mlungu ali nane
  • Hymn 954 Mbuye andipeza lero,
  • Hymn 385 Tsopano, poyamba paja,
  • Hymn 445 Mlewe oipawo,
  • Hymn 1363 Tamani Ambuye,
  • Hymn 51 Mbuye dalitsani Afrika,
  • Hymn 1410 Nthawi zonse mufunabe
  • Hymn 202 Timpemphere kutipatsa
  • Hymn 1273 Ndasiya zonse ndi Yesu kalelo,
  • Hymn 655 Ndiphunzitseni, Mbuyetu,
  • Hymn 918 Ntchito yonse yakeyo
  • Hymn 579 Pochezera m’dambomo,
  • Hymn 1016 Mbuye, mwatiuza ‘fe
  • Hymn 1121 Ndifuna Yesuyo,
  • Hymn 1124 Ndifuna Inu, Yesu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version