Hymn 417 M’manja a Yesu wanga December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 417 M’manja a Yesu wanga M’manja a Yesu wanga Ndilikugonamo, Mommo aphimba ine Nacho chikondicho. Mvera! Mudzera m’Mwamba Mawu a Yesu wanga; “Mwana, ndidzakusunga Pano pamtima panga.”