Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 379 MTSINJE woyerawo

  1. Home   »  
  2. Hymn 379 MTSINJE woyerawo

Hymn 379 MTSINJE woyerawo

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 379 MTSINJE woyerawo

 

MTSINJE woyerawo
Wotuluka m’nyumbayo
Ya Mlungu wathuyo
Uyeretse tonsefe.

Ife tifikeko
Tibatizidweko,
Tiyeretsedwedi
Ndi Ambuye leroli.

Mwa anthu onsewo
Umayenda mtsinjewu,
Nuŵachiritsadi
Okhulupirirawo.

Tikondwereratu
Pakumvera Yesuyo,
Abwere onsewo
Ndi kuloŵa m’mtsinjewu.

Post navigation

Previous: Hymn 360 KRISTU wakuyeratu,
Next: Hymn 381 MONGA zomera zonsezo

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 474 MPULUMUTSI, Mbusa wathu,
  • Hymn 391 MUNDIMVERE, Mbuye wanga
  • Hymn 817 Tibvomereze,
  • Hymn 435 ANAKWATIRA kale
  • Hymn 1753 Adzatipulumutsa
  • Hymn 378 Ku madzi ake odikha
  • Hymn 1827 Abramu kalelo anamvera bwino;
  • Hymn 251 NDIFUNA Yesuyo,
  • Hymn 673 Mbwere Mzimu Wakuyera,
  • Hymn 1318 Ndibwera kwa Ambuyeyo,
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 1522 Tikaona bvuto,
  • Hymn 401 Dzuwa la lero lonseli
  • Hymn 782 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 804 Muchotse zonse zoti bii
  • Hymn 233 AMBUYE Mulungu,
  • Hymn 952 Ndimayenda paulendo,
  • Hymn 175 Mlungu mverani, mphamvu patseni,
  • Hymn 943 Onse aliko takonda kalelo,
  • Hymn 600 Mbuye Yesu, myandikire,
  • Hymn 1644 Popachikidwa pa Golgotapo
  • Hymn 589 Koma ineyu
  • Hymn 525 Afike masiku
  • Hymn 145 MBIRI yakale lomwe
  • Hymn 691 Akukhala kunja,
  • Hymn 326 Yesu, Bwenzi la ochimwa,
  • Hymn 899 ‘Tate wa Kumwambako,
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 903 Iwo salekana, iwo salekana,
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 1505 Ndikampeza, ndikamtsata
  • Hymn 216 Ndi misozi ndi chisoni
  • Hymn 848 Mudze, mlowe m’mtimamu,
  • Hymn 1023 Kodi m’njiramo ndimvadi
  • Hymn 584 Ndi angelo,
  • Hymn 726 Mundidzze ndi chikondi,
  • Hymn 1606 Yesu, dzina lakufatsa,
  • Hymn 1302 Ndi inetu sinditha ‘yi
  • Hymn 1212 Zina ndi zinanso
  • Hymn 1683 Nsinga za imfa Iye ‘nadula,
  • Hymn 1813 Pochimwa anthu onsewo
  • Hymn 35 Zonse za m’dziko zidzatha,
  • Hymn 755 Pamene padzakhalapo
  • Hymn 796 Timvere Mawu anu
  • Hymn 874 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 332 Perekani mtima wanu,
  • Hymn 984 Mpingo wa Mulungu
  • Hymn 250 MBUYANGA Yesu,
  • Hymn 437 Yesu ndiye Mbusa,
  • Hymn 579 Pochezera m’dambomo,
  • Hymn 998 Anatilemba Yesu tikagwire nkhondo yake,
  • Hymn 1681 Mphamvu za imfa ndi za Satana
  • Hymn 1832 Za m’mdima, imfa, nkhondo ndi zoipa sindiopa;
  • Hymn 543 Kuli kaphiri m’talimo
  • Hymn 799 Inu Mlungu kalelo
  • Hymn 1194 Padziko lapansi
  • Hymn 1141 Pakulekana ifetu
  • Hymn 977 Musagonje, anthu inu,
  • Hymn 225 NDIDZAIMBA za Mulungu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version