Hymn 85 Mtima wanga wabvutika, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 85 Mtima wanga wabvutika, Mtima wanga wabvutika, Zaka zonse ndangochimwa; Tsono sindikangalika, ndingopuma mwa Yesu.