Hymn 85 Mtima wanga wabvutika, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 85 Mtima wanga wabvutika, Mtima wanga wabvutika, Zaka zonse ndangochimwa; Tsono sindikangalika, ndingopuma mwa Yesu.