Hymn 522 Akazi anadza December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 522 Akazi anadza Akazi anadza kwa Yesu ndi anawo, Anawaletsa anyamata nawakana ndithu; Ambuye nawapezadi, Anati: “Musatero ‘yi, Lolani ana abwere kwa Ine, Lolani ana abwere kwa Ine.