Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 522 Akazi anadza

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 522 Akazi anadza

 

Akazi anadza

kwa Yesu ndi anawo,

Anawaletsa anyamata

nawakana ndithu;

Ambuye nawapezadi,

Anati: “Musatero ‘yi,

Lolani ana abwere kwa Ine,

Lolani ana abwere kwa Ine.

Exit mobile version