Hymn 317 Zambiri zagona m’kholamo, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 317 Zambiri zagona m’kholamo, Zambiri zagona m’kholamo, Zosungika bwino ‘mo; Koma imodzi inasokeradi, Nitayika m’thengomo Kutali kuphiri loopsalo, Kutali ndi mbusa wakeyo.