Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu, Ona chikondi cha Mulungu, Ona zoipazo za anthu, Koma chakula ndi chikondi; Wapachikidwa Ambuyathu.