Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu, Ona chikondi cha Mulungu, Ona zoipazo za anthu, Koma chakula ndi chikondi; Wapachikidwa Ambuyathu.