Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

  1. Home   »  
  2. Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu

 

KALE m’mzinda wachifumu
Munalimo m’kholamo,
Momwe mkazi anaika
Mwana wake m’ndyeromo.
Ndiye mkaziyo Mariya,
Yesu Kristu Mwanayo.

Uyu ’natsikira kuno,
Mlungu Mbuye wathuyo;
Anabadwa uyu m’khola
Anagona m’ndyeromo.
Mwa osoŵa ndi oipa
Yesu anakhalamo.

Mwa ubwana wake wonse
Anakula m’mtima phee!
Anakonda, anafatsa,
Amay’ wake namvabe;
Ndipo ana nonsenu,
Mukamtsate bwinotu.

Ndipo Mwana uyu Yesu
Anakulakulabe;
Ndi wamng’ono ndi wofoka,
Anagona enawo.
Nsoni zathu anazimva
Ndi chimwemwe chathunso.

Ndi chifukwa atikonda,
Tidzampenya masowa,
Kuti Mwanayo wofatsa
Ndiye Mwini m’Mwambamo;
Atengera ana ake
Komwe adapitako.

Koma sitimpenya m’khola
Muli ng’ombe momwemo;
Ayi, tidzamwona m’Mwamba
Muli Mlungu ’Tatewo.
Ana akuyera mbuu
Adzamzunguliratu.

Post navigation

Previous: Hymn 456 ANA inu, ana inu,
Next: Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1224 Inde ndidzaimba nyimbo
  • Hymn 1251 Ndasokera m’tali ndithu
  • Hymn 227 NDIM’KONDE Kristuyo,
  • Hymn 186 MVERANI mbiri yozizwitsa
  • Hymn 456 ANA inu, ana inu,
  • Hymn 1220 Bwenzi ndinamkomanayo
  • Hymn 534 Bwerani, kondwerani,
  • Hymn 705 Tikhaletu nawo, Mbuye,
  • Hymn 926 Mbale wako unamkonda,
  • Hymn 771 Tsopano alandira
  • Hymn 19 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 829 Titamadi ‘Tate,
  • Hymn 497 Yesu andikonda ine,
  • Hymn 774 Tibatizidweko,
  • Hymn 865 Pakubweradi Woyesa tidzamlaka ifetu;
  • Hymn 809 Madzulo aja kalelo
  • Hymn 995 Taya zako zochenjera,
  • Hymn 1649 Kutenga inetu, kutenga inetu
  • Hymn 991 Ndi zapansi pano
  • Hymn 1686 Ndi mtima wonse mwimbedi
  • Hymn 1617 Anadzuka,
  • Hymn 470 Mutiletse tisaname
  • Hymn 328 Yesu ndiye mphamvu yanga,
  • Hymn 1107 Anthu onse pansi pano
  • Hymn 1134 Pansi pano ndili mlendo,
  • Hymn 267 Usekere moyo wanga,
  • Hymn 619 Tilimalima m’minda,
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 480 Tifunitsa Inu tere,
  • Hymn 1572 Mumbveke, mbveke, mbveke,
  • Hymn 558 Mwanayo wa Mulunguyo
  • Hymn 25 ANGELO amayimba,
  • Hymn 516 Zitsamba zakuyera
  • Hymn 1098 M’mene mantha andigwira,
  • Hymn 249 Amen, Amen, Amen.
  • Hymn 200 YESU mundimve, ndikuliratu,
  • Hymn 1705 Pa Iye padzapo
  • Hymn 1827 Abramu kalelo anamvera bwino;
  • Hymn 73 M’SANDIPITILIRE Yesu,
  • Hymn 322 PAKUYITANIDWA munthu pa dziko ino,
  • Hymn 1174 Sindinanyengedwa konse;
  • Hymn 744 Kristu ndi mwini moyo wathuwu,
  • Hymn 265 MUDZAZE Yesu mtima wanga ndi chikondicho,
  • Hymn 243 KONDWANI nonsenu,
  • Hymn 1726 Linadetsedwa dzuwa bii!
  • Hymn 739 Ndilibe wondithangata ‘ne ‘yi,
  • Hymn 217 CHIPULUMUTSO chathu chayandika,
  • Hymn 579 Pochezera m’dambomo,
  • Hymn 1228 Lindikomera dzina la Ambuye Yesu wanga,
  • Hymn 261 M’NDIYANDIKITSE nanu Yesu,
  • Hymn 1000 Amatininkha zida zoteteza mtima, ndizo:
  • Hymn 728 A! Yesu, ndapangana
  • Hymn 372 Potero onsewo
  • Hymn 949 Mundiwalire m’njira mwangamo,
  • Hymn 800 Yesu munadzukanso
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 171 IWE tiye, iwe tiye,
  • Hymn 133 Yesu watidzera, watidzera,
  • Hymn 927 Pakutsazikana nanu
  • Hymn 1289 Ndinasokeratu kutaliko,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version