Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

  1. Home   »  
  2. Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

 

ANTHU akum’maŵa
Nanka msangako,
Nzeru ’nali nazo,
Nafatsansowo;
Nanka kuli Mwana
Anabadwayo;
Anatsogozedwa
Ndi nyenyeziyo.

Anapeza Mwana
Ali m’kholamo,
Nagwadira Iwo
Mbuye wawoyo;
Anthu onse omwe
Ali pansipa,
Azitsata Mbuye
Ndi nyenyeziyo.

Mu ulemerero,
Yesu m’Mwambamo
Muli eni ake;
Anthu onsewo
Osadziŵa konse,
Akutalinso,
Akokedwe iwo
Ndi nyenyeziyo.

Akukhala kunja,
Osokeranso,
M’ŵaŵalire Mbuye,
Asagone’wo;
Amumdima omwe,
Olemedwanso,
Mtsogoleri wawo
Ndi nyenyeziyo.

Paulendo wathu
Tili pansipa,
Muŵalire tonse
Tili m’njiramo;
Mutitsogolere
Anthu tonsefe,
Mutifitse tonse
Ndi nyenyeziyo.

Post navigation

Previous: Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?
Next: Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1803 Nowayo nayendamo,
  • Hymn 155 Pemphero ndiko kufuna
  • Hymn 1340 Perekani mtima wanu
  • Hymn 1397 Okwawa pansi inu,
  • Hymn 297 Anapita nasiya
  • Hymn 434 CHIKONDI cha Mulunguyo,
  • Hymn 1145 Khalani duu! Mulungu wanuyu
  • Hymn 1760 Amithenga a Mulungu
  • Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa
  • Hymn 167 KODI mwalandira Yesu?
  • Hymn 1667 Yesu wakukoma mtima,
  • Hymn 973 Tigwire nkhondo yomwe
  • Hymn 1234 Ati Yesu Mbuyeyo:
  • Hymn 452 Tiana ife tingofoka,
  • Hymn 196 NDI inetu sinditha’yi
  • Hymn 329 Yesu atonthoza mtima
  • Hymn 376 Adzadalitsa ‘fe
  • Hymn 55 Ambiri tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 1205 Ndikonda chifukwa
  • Hymn 1220 Bwenzi ndinamkomanayo
  • Hymn 1265 Tere moyo wanga wonse,
  • Hymn 1295 Ambuye, mwazi wanuwo
  • Hymn 811 Wopulumutsa mudzetu;
  • Hymn 581 Mtiphunzitse bwinotu,
  • Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika,
  • Hymn 416 Woyenera ndani kunka
  • Hymn 882 Kodi tikulema nazo
  • Hymn 1569 Mtima wodetsa mukonzere,
  • Hymn 307 Atate Wamkulu ndi wamphamvu zonse,
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 1616 Anafera
  • Hymn 770 Atate, muwapenye
  • Hymn 1464 Nditama Nsembe ya Mulungu,
  • Hymn 1630 Anthu anu amafoka,
  • Hymn 1563 Mufike monga nyali younika m’mtimamo,
  • Hymn 462 Pothandiza amathu,
  • Hymn 494 YESU Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 63 POKUMBUKIRA mtandawo
  • Hymn 431 Pompano pandikonda
  • Hymn 1588 Wandiwombola inetu
  • Hymn 196 Tidzimba komweko nyimbo
  • Hymn 890 Kumbuka ‘bale ako
  • Hymn 1372 Zam’madzi zonse zakuopsyazo,
  • Hymn 1354 Mzimu Woyera, m’mtimamo
  • Hymn 433 Zoipa ndi zabwino
  • Hymn 646 Mudalitse nyumba yathu;
  • Hymn 1725 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 180 MALO alimo m’nyumba ya Yesu,
  • Hymn 1350 Mvera Yesu, mvera Yesu,
  • Hymn 536 Ana inu, myamikeni
  • Hymn 459 KALE anthu m’kholamo,
  • Hymn 203 NTHAWI yathadi bwerera mbale,
  • Hymn 1079 Khalatu woyera,
  • Hymn 221 Yesu and’itana,
  • Hymn 755 Pamene padzakhalapo
  • Hymn 651 Ikhale ngati nyali
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 1852 Mbuye ndamva mwawazira
  • Hymn 1579 Akhala mafumu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version