Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 239 TILI ndi mtendere

  1. Home   »  
  2. Hymn 239 TILI ndi mtendere

Hymn 239 TILI ndi mtendere

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 239 TILI ndi mtendere

 

TILI ndi mtendere
Wopambanatu,
Monga ngati mtsinje
Mumitimamo;
Koma mtsinje uno
Umayenda phee,
Nthaŵi zonse mtima
Nutonthozabe.

Tikakhulupira
Mlungu wathuyo,
Tidzaona mwayi
Ndi mtenderewo.

Dzanja la Mulungu
Litisunga nji!
Nkhondo ya Satana
Sitiopa ’yi.
Zaphokoso zonse
Ndi zoopsyazo
Sizibvuta mtima,
Siziloŵamo.

Masauko athu
Ndi zokondwazo,
Azilola zonse
Ndi Atatewo.
Pokhulupirira
Tidzapezabe
Kuti mtima wake
Utikonda ’fe.

YESU ndiye Mbuye wanga,
Ndamva Mawu akewo
Andilandira ine,
Nandipulumutsatu.
Mwalembedwa mukalata
Mawu ake omwewo,
Kuti iwo akumvera
Akalandiridwatu.

Ndinakahala wakuipa, Ndinamkana kalelo;
Koma Yesu waiŵala
Mphulupulu zangazo.

Wapumitsa mtima wanga,
Kaamba ndaphunziratu
Mau ake olembedwa
Mukalata mwakemo.

Mumvetu abwenzi athu,
Musakanirire ’yi;
Yesu aitana inu,
Zalembedwa zomwezi.

Post navigation

Previous: Hymn 238 MULUNGU wanga,
Next: Hymn 240 YESU ndiye Mbuye wanga,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 209 M’NDILANDIRE ine Mbuye
  • Hymn 416 Woyenera ndani kunka
  • Hymn 365 DZUŴA lapita,
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 1319 Ambuye naitana ‘ne:
  • Hymn 1142 Tidzathawira kuti ‘fe
  • Hymn 733 Ndimamva ludzu Yesu,
  • Hymn 1457 Ndidziwa kuti Yesu
  • Hymn 1282 Ndilinkudza kwa Ambuye,
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 1454 Ambuye, musendeze
  • Hymn 1713 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 924 Kodi uli ndi chisoni
  • Hymn 953 Ichi chindisangalatsa
  • Hymn 1596 Anamnyoza pansi pano,
  • Hymn 1246 Ambuyanga, ndalephera,
  • Hymn 337 ‘Tate ‘Nu,
  • Hymn 1497 Simbani mobwereza,
  • Hymn 308 Ifetu kuchimwa, Mbuye,
  • Hymn 260 ODALA ndi onsewo,
  • Hymn 847 Konse kuli mdima bii
  • Hymn 427 AULENDO amayenda
  • Hymn 1156 Imfa ndi manda sitiopa ‘yi,
  • Hymn 467 Ife ana sitiopa,
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 1816 Anatikondakonda ‘Ye,
  • Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
  • Hymn 1213 Mwamva Yesu m’mtimamo,
  • Hymn 1838 Ndiye Mbuye wa ambuye;
  • Hymn 1342 Tadza kumtsinjeku
  • Hymn 493 DZUŴA li
  • Hymn 1394 Paphiri ndi padambo
  • Hymn 351 CHIYEMBEKEZO changacho,
  • Hymn 607 Dziko lonse lilikukondwa, mlengalenga mpheponso,
  • Hymn 1203 Zambiri zangazo
  • Hymn 1047 Ambuye, chotsani zonse zomwezo
  • Hymn 264 KHALATU woyera, pempheratu m’tseri;
  • Hymn 500 Mbuye Yesu andisunga
  • Hymn 1491 Zokandweretsa m’dzikomu
  • Hymn 1447 Yesu ngwachifundodi,
  • Hymn 1537 Mulowe m’mtima, mdzazetu
  • Hymn 386 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 1744 Kale ophunzira ake
  • Hymn 804 Muchotse zonse zoti bii
  • Hymn 475 MZINDA woyerawo
  • Hymn 1043 Mbiri yake ubukitse,
  • Hymn 1253 Ndingopatsa Inu Mbuye
  • Hymn 336 Perekani mtima wanu
  • Hymn 75 MBUYE, mutsaganetu
  • Hymn 947 Akristu tonsefe, tikondwe m’Dzikoli
  • Hymn 1385 Anatsogolera kale
  • Hymn 964 Kodi simuona njira,
  • Hymn 1707 Andiferatu ‘Ye,
  • Hymn 1532 Mubwere kuno Mzimu ‘Nu,
  • Hymn 926 Mbale wako unamkonda,
  • Hymn 314 E, moto wanu woyera
  • Hymn 1509 Mkate wamoyowo
  • Hymn 768 Ndi ife tinga mbewuzo
  • Hymn 179 Ndinachimwa poganiza

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version