Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 95 TAMANI mphamvu ya Yesu,

  1. Home   »  
  2. Hymn 95 TAMANI mphamvu ya Yesu,

Hymn 95 TAMANI mphamvu ya Yesu,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 95 TAMANI mphamvu ya Yesu,

 

TAMANI mphamvu ya Yesu,
Angelo agwade;
Angelo agwade;
Tulutsanitu korona,

Mumveke, mveke, mveke,
Mveke, mveke, mveke,
Mveke Mbuyeyo!

Inu osankhidwa ake,
Owomboledwa ’Nu,
Owomboledwa ’Nu,
Tamani Mpulumutsiyo,

Anthu onse ndi mitundu
Pa dziko linotu,
Pa dziko linotu,
Am’lemekeze Mfumuyo.

Tifuna kuti komweko
Tikam’gwadire ’Ye;
Tikam’gwadire ’Ye;
Tidzayimba kosaleka.

Post navigation

Previous: Hymn 94 KHAMULO liliko
Next: Hymn 96 MTIMA wanga uyamiketu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 688 Anthu akum’mawa
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 188 MPULUMUTSI Wokondedwa,
  • Hymn 94 KHAMULO liliko
  • Hymn 749 Ndiye wodyetsa anthu omwewo,
  • Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?
  • Hymn 785 Yehova adalitse ‘nu,
  • Hymn 846 Kristu wakuyeratu,
  • Hymn 734 Ndi mkate wanu, Yesu
  • Hymn 987 Ambuye wa Kumwamba,
  • Hymn 222 Ndilikudzatu,
  • Hymn 572 Anadza nazo mphatso zake
  • Hymn 145 MBIRI yakale lomwe
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 1767 Ndiye anayang’ana
  • Hymn 109 MUTHIRE, Yesu, m’mtimanga
  • Hymn 1355 Atate, Mwana, Mzimunso,
  • Hymn 1602 M’mawu a Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 775 Mwa anthu onsewo
  • Hymn 848 Mudze, mlowe m’mtimamu,
  • Hymn 1419 Amayi ‘nu, amayi ‘nu,
  • Hymn 662 Tisaleme pakuchita zabwinozi,
  • Hymn 299 “Posunga nkhosa ife
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 796 Timvere Mawu anu
  • Hymn 878 Zokoma inde nthawizi
  • Hymn 400 ONA Mwana wa Nkhosa,
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 1164 Tikakhulupira
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 1621 Yang’anani anthu onse,
  • Hymn 504 Pakumyamika Iye
  • Hymn 1718 Ona chikondi cha Mulungu,
  • Hymn 1460 Akuti anthu akumvera
  • Hymn 206 Uzanitu abale,
  • Hymn 107 Panalibe mwa abale
  • Hymn 132 MVERA mtima wanga ’we
  • Hymn 225 NDIDZAIMBA za Mulungu,
  • Hymn 1838 Ndiye Mbuye wa ambuye;
  • Hymn 1138 Masiku onse m’mtima mwanga
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 1756 Mwana, adzakuyesa
  • Hymn 1731 Ife tinachimwadi,
  • Hymn 433 MULUNGU wa Kumwamba bwera kunoku
  • Hymn 353 Anatuma Mtetezi,
  • Hymn 231 AMBUYE, m’imfamo
  • Hymn 206 YESU, mulikundipempha
  • Hymn 781 Tatsegukani inutu,
  • Hymn 676 Adze amitundu yonse,
  • Hymn 469 NDIKONDA mbiri yomwe
  • Hymn 419 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 307 Atate Wamkulu ndi wamphamvu zonse,
  • Hymn 1335 Wandifera Yesuyo
  • Hymn 486 MPULUMUTSI Yesu,
  • Hymn 1606 Yesu, dzina lakufatsa,
  • Hymn 315 YENDANI munjira yake,
  • Hymn 1477 Anena anthu onsewo,
  • Hymn 149 Ndisauka, sindikhoza

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version