Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo

  1. Home   »  
  2. Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo

Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo

 

Wolenga ndi Yemweyo

Wa zinthu zonse zathu;

Maudzu ameretsa,

Nayatsanso nyenyezi.

Mphepozo zonse zimva,

Nyamazo aziweta;

Sadzaiwala konse

Anake kuwadyetsa.

Post navigation

Previous: Hymn 620 Mphatso zonse zathu
Next: Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 425 Ine ndine mlendo
  • Hymn 344 M’watame,
  • Hymn 592 Kuti m’Mwambamo
  • Hymn 45 Malawi dziko lokongola,
  • Hymn 1535 Lichepa dontho lokhali,
  • Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu
  • Hymn 1050 Ndafoka inetu,
  • Hymn 1013 Tizifesa m’dzuwa,
  • Hymn 1404 “Undipatsetu
  • Hymn 1374 Inu mumvere anyamatawo,
  • Hymn 114 NDIPO Eliya anati kwa Elisa:
  • Hymn 242 M’mene mubwera
  • Hymn 278 TITHAŴIRENJI ifetu
  • Hymn 1613 A Mulungu
  • Hymn 1353 Ambuye Yesu, Inutu
  • Hymn 1807 Chithawa m’talitali
  • Hymn 54 Dalitsani mafuko onse,
  • Hymn 1816 Anatikondakonda ‘Ye,
  • Hymn 173 Mema nkhondoyo, wadza mdaniyo,
  • Hymn 626 Inde, ‘Tate, mtiyendetse
  • Hymn 314 TIYENI nonsenu okonda YESUYO,
  • Hymn 431 AKAPANDA kumanga,
  • Hymn 458 USIKUWO, woyerawo!
  • Hymn 979 Limbikani inu nonse,
  • Hymn 1349 Salephera, salephera,
  • Hymn 433 MULUNGU wa Kumwamba bwera kunoku
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 947 Akristu tonsefe, tikondwe m’Dzikoli
  • Hymn 1387 Amaweta nyama zonse,
  • Hymn 188 MPULUMUTSI Wokondedwa,
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 87 Aleluya, mwandigula,
  • Hymn 1293 Chitsimecho cha mwaziwo
  • Hymn 1479 Ndi Yesu yemwe kalelo
  • Hymn 7 “Mbuye Woyera! E, Woyeranokha!
  • Hymn 900 Mutipatse leroli
  • Hymn 1632 Ndi chiyembekezo ichi
  • Hymn 1839 Yehova ndiye Mbusa wanga sin’ngasowe konse;
  • Hymn 1654 Mbuye, mutsaganetu
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 876 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 1325 Maiwe! Thanthwe long’ambikatu,
  • Hymn 1018 Yesu afuna iwe unnke kwawoko,
  • Hymn 967 Mbuye, ndapangana
  • Hymn 427 AULENDO amayenda
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 281 Atate, ndipempha
  • Hymn 255 Pakuona imfayo
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 170 YESU ponong’oneza, idzanitu;
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 1469 M’kufatsa kwake komwe
  • Hymn 1231 Nlokoma dzinalo la Yesu, ndilo thanthwe langa,
  • Hymn 1544 Wakunga mwana ine,
  • Hymn 92 Ufuna kugwira ntchito yake?
  • Hymn 488 M’MANJA a Yesu wanga
  • Hymn 392 Chimwemwe chomwe mpatseko
  • Hymn 1578 Onsewa ‘nachimwa

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version