Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

  1. Home   »  
  2. Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 214 KUNALI munthu ku Yeriko,

 

KUNALI munthu ku Yeriko,
Dzina lake Zakeyu;
Anali munthu wamkulu,
Wokhometsa misonkho.

(M) Kunali Zakeyu,
(O) Ku Yeriko,
(M) Nafunafuna,
(O) Kuwona Yesu,
(M) Koma chifukwa,
(O) Cha khamulo,
Anakwera mumtengo.

Paulendowo Ambuyeyo,
Anafika pamtengo;
Nayang’ana m’mwamba muja,
Anawona Zakeyu,

Ambuye Yesu nanenadi,
“Fulumira nutsike;
Lero lino ndiyenera,
Kukhala m’nyumba mwako.”

Zakoyuyo mofulumira,
Anatsika mumtengo,
Anam’tenga Mbuye Yesu,
Kuti akam’chereze,

Anadandauladi ena,
“Ambuye wachitanji?
Bwanji Iye analowa,
M’nyumba ya wochimwayo?”

Zakeyuyo pakumva ichi,
Anawuza Ambuye:
“Theka la chuma changacho,
Ndidzapatsa osowa.”

Leronso chipulumutsochi,
Chagwera m’nyumba yathu;
Tilape zoipa zathu,
Kutí tipulumuke.

Post navigation

Previous: Hymn 200 YESU mundimve, ndikuliratu,
Next: Hymn 221 A! CHIKONDI chopambana,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1148 Ndiimba mumtima mokondwa
  • Hymn 654 Ndilimbikitse, Mbuye, nji!
  • Hymn 419 ANYAMATA a Mulungu,
  • Hymn 166 NDICHITENJI kukapeza
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 965 Mundiuze, aulendo,
  • Hymn 1560 Mthandizi ndinu, mndithangate ine
  • Hymn 1454 Ambuye, musendeze
  • Hymn 1502 Kodi ulikulemedwa
  • Hymn 1493 Mbiri yakalelomwe
  • Hymn 912 Makomo afanana
  • Hymn 172 TADZA kukudyaku,
  • Hymn 58 PAMTANDAPO Ambuyeyo
  • Hymn 442 Posachedwa tilekana
  • Hymn 21 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 850 Pemphero, pemphero,
  • Hymn 1477 Anena anthu onsewo,
  • Hymn 1304 Ndi ine sizitheka ‘yi
  • Hymn 1729 Munthu Wazisoniyo
  • Hymn 255 KHALA chete mtima wanga
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 244 Ndidze pafupi pa
  • Hymn 424 Yesu, mndiyeretse,
  • Hymn 1259 Ndikhulupirira bwino
  • Hymn 1402 Mverani Iye ati: idzanitu;
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 504 Pakumyamika Iye
  • Hymn 507 Yesu ndimkonda, akondanso ine,
  • Hymn 141 TAONANI pamtandapo,
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 89 Muli mphamvu yodabwitsatu
  • Hymn 321 PAKUONA imfayo
  • Hymn 899 ‘Tate wa Kumwambako,
  • Hymn 1166 Masauko athu
  • Hymn 1127 Mbuyanga Yesu, mundigwire dzanja;
  • Hymn 251 Kuli chimwemwe m’dzuwalo
  • Hymn 303 MEMA nkhondoyo, wadza mdaniyo,
  • Hymn 472 Amakumbukira zonse
  • Hymn 1426 Wina panalibe
  • Hymn 313 MUNDIŴALIRE m’njira mwangamo,
  • Hymn 645 Kristu ndiye mwala wathu,
  • Hymn 242 M’mene mubwera
  • Hymn 1686 Ndi mtima wonse mwimbedi
  • Hymn 738 Mommuno, Mbuye, mkate wanuwu,
  • Hymn 435 ANAKWATIRA kale
  • Hymn 816 Mdima wafika,
  • Hymn 598 Mlungu ali nane;
  • Hymn 727 Imfa ikandifikira,
  • Hymn 324 TIKAGWIDWA ndi chisoni,
  • Hymn 384 Mulungu akhale nawo
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 242 NDIIMBA mumtima mokondwa,
  • Hymn 131 Lolani ana, mumve Mlungu,
  • Hymn 1134 Pansi pano ndili mlendo,
  • Hymn 1798 Mukondwe anthu a Mulungu,
  • Hymn 798 M’nyumba yanu, Mlungu, ‘yi
  • Hymn 1782 Poyamba paja analenga
  • Hymn 1575 Tifuna kuti komweko

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version