Chichewa Christian Hymns
Hymn 163 MALO anachepa,
MALO anachepa,
Nyumba anammana,
Agona m’modyera,
Mutu paudzuwo.
Anthu sanamtama,
Nyimbo panalibe,
M’nyumba ya alendo
Malo munalibe.
Apempha malo Ambuye;
E, mlandiretu m’mtimamo,
Ungamvetu Kumwambako,
“Akusowanso malo.”
Wina panalibe
Kumlandira Iye,
Wakumsangalatsa,
Wamkonda nasowa.
Anthu sanafuna
Chuma chosatha,
Sanamkondwere