Hymn 793 Tikondwera kuti December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 793 Tikondwera kuti Tikondwera kuti Tipumula lero; Tazileka ntchito Kuti tipemphere. Koma ntchito zathu Zapa lero lino Nzakumvera Yesu, Kumlandira bwino.