Hymn 689 Anapeza Mwana December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 689 Anapeza Mwana Anapeza Mwana Ali m’kholamo, Namgwadira Iwo Mbuye wawoyo; Anthu onse omwe Ali pansipa, Azitsata Mbuye Ndi nyenyeziyo.