Hymn 689 Anapeza Mwana treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 689 Anapeza Mwana Anapeza Mwana Ali m’kholamo, Namgwadira Iwo Mbuye wawoyo; Anthu onse omwe Ali pansipa, Azitsata Mbuye Ndi nyenyeziyo.