Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 517 “Osana m’Mwambamwamba!”

  1. Home   »  
  2. Hymn 517 “Osana m’Mwambamwamba!”

Hymn 517 “Osana m’Mwambamwamba!”

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 517 “Osana m’Mwambamwamba!”

 

“Osana m’Mwambamwamba!”

Nyimboyi t’iimbenso,

Pokhala Kristu Mfumu

Ndi Mpulumutsiyo.

Timtamandire Iyeyu

Ndi mtima wonsewo;

Tipite kwawo komwe

Tikaimbirenso.

Post navigation

Previous: Hymn 500 Mbuye Yesu andisunga
Next: Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 23 Mvera mtima wanga ‘we
  • Hymn 1460 Akuti anthu akumvera
  • Hymn 1587 Nditama Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 328 KULIBE vuto
  • Hymn 53 AMBUYE Yesu anamva chisoni,
  • Hymn 1341 Tadza kukudyaku,
  • Hymn 1029 Nkhawa tilibe; Yesuyo
  • Hymn 896 Mbuye, ndinalema ine,
  • Hymn 296 Mngelo anatumidwa
  • Hymn 1426 Wina panalibe
  • Hymn 446 Yesu alandira
  • Hymn 906 Mulibe zoipa m’Dzikolo,
  • Hymn 1240 Ndilikuva m’mtima mwanga
  • Hymn 154 Pemphero ndiko kulira,
  • Hymn 95 Palibe mmodzi akanatha
  • Hymn 134 INU ansembe ngakhale mufunsa,
  • Hymn 650 Tikondwa tonse ndi kukuthokazani Nu
  • Hymn 1317 Ambuye naitana ‘ne:
  • Hymn 1572 Mumbveke, mbveke, mbveke,
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 16 MTIMA wanga lemekeza,
  • Hymn 1315 Ambuye ‘naitana ‘ne:
  • Hymn 429 M’DZANJA lanu Ambuye,
  • Hymn 22 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 1756 Mwana, adzakuyesa
  • Hymn 927 Pakutsazikana nanu
  • Hymn 96 MTIMA wanga uyamiketu,
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 73 M’SANDIPITILIRE Yesu,
  • Hymn 195 Bwinoli tipita,
  • Hymn 829 Titamadi ‘Tate,
  • Hymn 319 NDIDZATANI ine,
  • Hymn 1513 M’Bukuli ine ndi
  • Hymn 15 YEHOVA ndiye Mbusa wanga,
  • Hymn 1190 Aleluya, mlemekeze,
  • Hymn 461 Inu nonse anzanga,
  • Hymn 65 NLA Mlungu dzuŵali:
  • Hymn 1176 Sandinyenga, salephera;
  • Hymn 122 Musadziunjikire chuma cha padziko,
  • Hymn 107 MUBWERE kuno Mzimu ’Nu
  • Hymn 1516 Pakudera nkhawa ‘ne,
  • Hymn 840 Ambuye munapatsa tsiku
  • Hymn 297 POKUMANA m’mayesero a dziko lino,
  • Hymn 1241 Ati: Mwana, kumbukira
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 14 MTIMA wanga uyamike,
  • Hymn 544 Zoopsya sitidziwapo
  • Hymn 1324 M’moyo uno kunsiku
  • Hymn 498 Yesu akonda,
  • Hymn 377 Yehova, Mbusa wangadi,
  • Hymn 1071 Kumwamba Yesu mthandize,
  • Hymn 499 TIKUTHA kupemphera,
  • Hymn 1283 Yesu ndikhulupirira
  • Hymn 1254 Mukhululukire ine,
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 908 Ndikonda kuganizirabe
  • Hymn 574 A! Yesu Mbuye wakuyera,
  • Hymn 1593 Wina atikonda ife,
  • Hymn 1079 Khalatu woyera,
  • Hymn 777 Mulungu ali muno,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version