Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

  1. Home   »  
  2. Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

 

MBUYE wathu, mutipatsa
Zonse tili nazozo,
Mutikomeratu mtima
Osaleka konseko,
Mutikonda, mutisunga,
Mutisamalira ’fe.

Dzuŵa, madzi, kudya, mpweya,
Moyo, zonse nzanuzi,
Si za ife, nzaulere,
Tingozilandiradi;
Zifumira kwa Aate
Wotikondakondatu.

Monga tilandira, Mbuye,
Mtiphunzitse tonsefe
Tipere chuma chathu
Ndi kusangalalatu;
Zakukhala m’manja mwathu
Tiziyese nzanudi.

Tikhaletu nawo, Mbuye,
Mtima wosauma ’yi
Ndi wofatsa ndi wabwino
Ndi woyerayeradi,
Kuti tiyenere Dzina
La Mbuyathu Yesuyo.

Tisaiwalire ’bale
Athu osadziŵa ’Nu,
Akulira ndi odwala
Tiŵapemphereratu;
Titsanzenso Mbuye Yesu
Ndi k’ŵathangatira ’wo.

Dalitseni, Mbuye, zonse
Zomwe taperekazi,
Mzilandire, nsembe yathu,
Mziyeretse Inudi
Ndi mitima yathu yonse
Tikuyamikirani.

Post navigation

Previous: Hymn 380 ATATE, muwapenya
Next: Hymn 401 A MULUNGU,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1450 Ndi angelo akumwamba
  • Hymn 737 Mommuno, Mbuye, tionanetu,
  • Hymn 43 Ulendo wathu ukadzatha
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 1516 Pakudera nkhawa ‘ne,
  • Hymn 922 Onse akulapawo
  • Hymn 1540 Pankhope pathu mthirepo
  • Hymn 203 Pamtandapo, pamtanda,
  • Hymn 611 Tidzakhala naye nthawi zonse ndi kuimbako,
  • Hymn 1084 “Khala mwa Ine,” munachotsa tsoka,
  • Hymn 59 IMVANI uthenga,
  • Hymn 1197 Ndafoka ine kale,
  • Hymn 1604 Yesu, dzina lakukonda,
  • Hymn 1548 Mtitsitsimutse ife
  • Hymn 1246 Ambuyanga, ndalephera,
  • Hymn 1063 Pokhala mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 683 Musamaopa kanthu ‘yi, tamani Yesuyo;
  • Hymn 549 Ndiye Mbuye, Mfumu yanga,
  • Hymn 1840 Ndiye M’busa wanga,
  • Hymn 1304 Ndi ine sizitheka ‘yi
  • Hymn 1007 M’mene umauka m’mawa,
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 817 Tibvomereze,
  • Hymn 540 Amithenga akumwamba
  • Hymn 558 Mwanayo wa Mulunguyo
  • Hymn 227 NDIM’KONDE Kristuyo,
  • Hymn 1556 Mzimu Woyera, mudzetu kwa ine,
  • Hymn 210 Nyumba yodyera ilikudzaza;
  • Hymn 92 Ufuna kugwira ntchito yake?
  • Hymn 1734 “Senzani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 1203 Zambiri zangazo
  • Hymn 1771 Iye natsitsa kunsi
  • Hymn 199 Watitsogolera Mbuye,
  • Hymn 349 Aitana,
  • Hymn 1829 Mulungu ndiye Mbusa wanga, sindisowa konse;
  • Hymn 1093 Odala ndi onsewo
  • Hymn 1812 Kuzani Mlungu m’Mwambamo,
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 81 MBUYE Yesu adzabwera,
  • Hymn 742 Tikadya phando zaka zonsezi,
  • Hymn 133 Yesu watidzera, watidzera,
  • Hymn 1662 Msandipitire, Yesu,
  • Hymn 1813 Pochimwa anthu onsewo
  • Hymn 373 NYUMBA ya Mulungu, ili pano,
  • Hymn 699 Inu wakudzatu
  • Hymn 1505 Ndikampeza, ndikamtsata
  • Hymn 281 Atate, ndipempha
  • Hymn 1728 Zofuna zanga zonsezo
  • Hymn 701 Inu Atatuwo,
  • Hymn 283 Ndalema ndathodwa
  • Hymn 395 Usiku uno mutisungedi,
  • Hymn 940 Ndamvatu kuti tifika komweko
  • Hymn 1106 Mlungu ndi wachikhalire.
  • Hymn 675 Pamaiko pali mdima,
  • Hymn 174 Haya, anzathu, itilinda nkhondo;
  • Hymn 897 Ndine mlendo pansi pano,
  • Hymn 798 M’nyumba yanu, Mlungu, ‘yi
  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version