Hymn 239 Akumwambawo December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 239 Akumwambawo Akumwambawo Naimbitsatu Kukulemekezani; Koma monga mwana M’dziko munabadwa, Munadzichepetsadi.