Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 5 ATATE wa Kumwambako,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 5 ATATE wa Kumwambako,

 

ATATE wa Kumwambako,
Munawombola ife, ndi
Chikondi chanu chijacho;
Tiyamikira Inutu.

Ambuye Yesu Inutu,
Munabadwira anthu ’fe;
Munatifera tonse ’fe;
Tiyamikira Inutu.

Mzimu Woyera m’mtimamo
Tiyeretsedwe ndi Inutu;
Munatisunga bwinoli,
Tiyamikira Inutu.

Atate, Mwana, Mzimunso,
Ndinu Atatu, Mmodzitu
Ochimwa tikupemphani:
Mutikhululukire’fe

Exit mobile version