Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,

 

MAWU akewo anamveka ponse,
Olalikidwa ndi aneneriwo;
Kuti yense wakumvera mawuwo,
Apulumuke.

(Mawuwo) Amveke,
(Tu) Kwa onsewo;
(Wo) Muetseratu ‘we sadzafa ndithu.

Tamveratu ‘we Mawu a Mulungu,
Khulupilira mwa
Ambuye Yesu;
Udzalandira moyo wosathawo,
Udzakondwera.

Tsoka kwa iye wosakhulupira,
Zolalikidwa ndi aneneriwo;
Koma patsiku la chiŵeruziro,
Adzafa ndithu

Exit mobile version