Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 199 NDINASOKERA kutali,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 199 NDINASOKERA kutali,

 

NDINASOKERA kutali,
Ndinadya ndi nguluwe,
Ndinakhala mu zoipa,
Chifukwa ndinachimwa.

Mmene ndafika
kwa ‘tate,
Nandikonzeratu phwando;
“Tidye tisekere naye,
Mwanayu anasowa.”

Koma mkulu wanga ndiye,
Sanandirandiretu;
Sanafune tate wanga,
Andikhululukire.

Ambuye amayitana,
Anthu onse ochimwa;
Kuti adzetu kwa Iye,
Kumene kuli moyo.

Exit mobile version