Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 412 MOYO uli pafupi,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 412 MOYO uli pafupi,

 

MOYO uli pafupi,
Monga kugwa kwa tsamba,
Ndikumanga mitolo kangaza;
Usachedwe m’zoipa,
Sudzapeza mpumulo;
Ndipo sadzakuyankha,
Kangaza.

Kangaza, kangazatu,
Yesu ali kuyitana, kangaza;
Usachedwe m’zoipa,
Sudzapeza mpumulo;
Ndipo sadzakuyankha,
Kangaza.

Unyamata ngovuta,
Umabwera nupita,
Ndipo sadzakuyankha kangaza;
Usachedwe m’zoipa,
Sudzapeza mpumulo;
Ndipo sadzakuyankha
Kangaza.

Exit mobile version