Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 297 POKUMANA m’mayesero a dziko lino,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 297 POKUMANA m’mayesero a dziko lino,

 

POKUMANA m’mayesero a dziko lino,
Matenda, imfa ndi usiwa;
Moyo umalefuka,
Ndikugwetsedwa mphwayi;
Mpaka nditamuuza Yesuyo.

Um fotokozere Yesu vuto lako,
Um fotokozere Yesu zonsezo;
Um’fotokozere Yesu vuto lako;
Adzakuchitira chifundo.

Pokumana m’mayesero a dziko lino,
Ndinasokera kutaliko;
Yesu nandigwira dzanja,
Nanditsogolera;
Mmene ndinamuuza zonsezo.

Abale tisachedwe ndi za dziko lino,
Za dziko lino ndi zachabe;
Yesu akufuna tibwere kwa Iye lero,
Kuti timuuzetu zonsezo.

Exit mobile version