Chichewa Christian Hymns
Hymn 25 ANGELO amayimba,
ANGELO amayimba,
Nyimbo zawo,
M’mwambamo.
Kulemekeza Mlungu,
Waulemelero.
(B) Poyimba atero,
(O) Aleluya,
(B) Mulungu wathu,
(O) Aleluya,
(B) Wopambanayo,
(O) Aleluya Aleluya,
Kwa Mulungu
Wa M’mwamba.
Ifenso timayimba,
Nyimbo zathu, pansipa;
Kulemekeza Mlungu,
Waulemelero.
