Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 217 CHIPULUMUTSO chathu chayandika,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 217 CHIPULUMUTSO chathu chayandika,

 

CHIPULUMUTSO chathu chayandika,
Padziko lapansi;
Lapa msanga nthawi yako yatha,
Moyo wako uthanso.

(M) Inetu, sindine ndekha,
(O) Tawomboledwa;
(M) Inetu, sindine ndekha,
(O) Tawomboledwa;
Ngakhale,
Nyanja ndi dziko,
Zonsezi zawomboledwa.

Kodi mbale wanga uchedweranji?
Padziko lapansi;
Fulumira nthawi yako yatha,
Moyo wako uthanso.

Yesu ndiye pothawiratu. ife,
Padziko lapansi;
Lapa msanga nthawi yako yatha,
Moyo wako uthanso.

Exit mobile version