Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 203 NTHAWI yathadi bwerera mbale,

Chichewa Christian Hymns

Hymn 203 NTHAWI yathadi bwerera mbale,

 

NTHAWI yathadi bwerera mbale,
Ona dzuwa lapendekadi;
Bwereradi, bwereradi,
Ona Yesu akuyitana.

Bwerera mwana wanga,
Bwerera;
Utsate chiyero changa zedi,
Bwerera, mwana wanga
Bwerera;
Utsate chiyero zedi.

Siya zoipa bwerera msanga,
Ona dzuwa lapendekadi;
Bwereradi, bwereradi,
Ona Yesu akuyitana.

Exit mobile version