Hymn 19 MULUNGU akhale nawo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Christian Hymns Hymn 19 MULUNGU akhale nawo, MULUNGU akhale nawo, Ulemerero ndi dalitso; Ndiye Atate, Mwana, Mzimu Woyera, Mlungu mmodzi. Tsopano, poyamba paja, Masiku onse alinkudza; Mphamvu, ulemerero, Dalitso, chipambano.