Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 999 Amaliwongo ochuluka amalowa m’mtima
Amaliwongo ochuluka amalowa m’mtima
Nafuna kuipitsamo usana ndi usiku;
Tikatsatabe Mfumu yathu sitidzagwa konse,
Pakuti atipatsa mphamvu tipambane nazo.