Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 992 Mukandipweteka,
Mukandipweteka,
Ndipirirapo;
Nsembe yanga ndiyo,
Landirani ‘yo.
Ndikachita mantha
Sindithawa ‘yi;
Mtima udzalimba,
Ndidzaima nji!
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 992 Mukandipweteka,
Mukandipweteka,
Ndipirirapo;
Nsembe yanga ndiyo,
Landirani ‘yo.
Ndikachita mantha
Sindithawa ‘yi;
Mtima udzalimba,
Ndidzaima nji!