Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 991 Ndi zapansi pano
Ndi zapansi pano
Ndikokedwadi,
Koma ndi chisoni
Mndiphunzitsedi;
Ndisaiwalire
Za Getsemane,
Pena mtanda wanu
Yesu Mbuye ‘Nu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 991 Ndi zapansi pano
Ndi zapansi pano
Ndikokedwadi,
Koma ndi chisoni
Mndiphunzitsedi;
Ndisaiwalire
Za Getsemane,
Pena mtanda wanu
Yesu Mbuye ‘Nu.