Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 988 Ndikhumba Mzimu wanu
Ndikhumba Mzimu wanu
Kundiyeretsa mbuu!
Pang’ono ndi pang’ono
Mundiphunzitsetu;
Ndifuna nzeru zanu
Zakundifitsako
Kumwamba kuli Inu,
Ambuye wangayo.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 988 Ndikhumba Mzimu wanu
Ndikhumba Mzimu wanu
Kundiyeretsa mbuu!
Pang’ono ndi pang’ono
Mundiphunzitsetu;
Ndifuna nzeru zanu
Zakundifitsako
Kumwamba kuli Inu,
Ambuye wangayo.