Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 987 Ambuye wa Kumwamba,
Ambuye wa Kumwamba,
Mundithangatetu
Kuyenda bwino lomwe
M’elendo unowu.
Kawiri ndi kawiri
Ndipunthwa m’njiramo;
Mlimbitse mtima wanga,
Ndingatayikeko.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 987 Ambuye wa Kumwamba,
Ambuye wa Kumwamba,
Mundithangatetu
Kuyenda bwino lomwe
M’elendo unowu.
Kawiri ndi kawiri
Ndipunthwa m’njiramo;
Mlimbitse mtima wanga,
Ndingatayikeko.