Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 974 Tsopano timenyana
Tsopano timenyana
Ndi zakuipazi;
Pamene nkhondo yatha
Tidzanka kwathuko.
Yesu adzalandira
Ankhondo ake onse;
Adzakhalira naye
Kumwamba komweko.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 974 Tsopano timenyana
Tsopano timenyana
Ndi zakuipazi;
Pamene nkhondo yatha
Tidzanka kwathuko.
Yesu adzalandira
Ankhondo ake onse;
Adzakhalira naye
Kumwamba komweko.