Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 971 Ndinu Mbusa wanga;
Ndinu Mbusa wanga;
Mndithandizetu;
Ndisaipse nazo
Mtima wangawu.
Osaoopa konse,
Osachimwa ‘yi.
Mndiyendetse Yesu
M’njira yanuyi.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 971 Ndinu Mbusa wanga;
Ndinu Mbusa wanga;
Mndithandizetu;
Ndisaipse nazo
Mtima wangawu.
Osaoopa konse,
Osachimwa ‘yi.
Mndiyendetse Yesu
M’njira yanuyi.