Hymn 970 Pena kumwa nawo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 970 Pena kumwa nawo, Pena kumwa nawo, Ndisateroko, Pena kukaona Gule woipa, Pena kuwombeza Sindifuna ‘yi; Yesu mndithandize Kuzikanazi.